Deuteronomy 3:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake tidapitirira ulendo kulunjika ku Basani. Mfumu Ogi pamodzi ndi anthu ake onse, adatuluka kudzatithira nkhondo pafupi ndi mudzi wa Ederei.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo tinatembenuka, ndi kubwera kunka njira ya ku Basani; ndipo Ogi mfumu ya Basani anatuluka kukomana nafe, kugwirana nafe nkhondo, iye ndi anthu ake onse, ku Ederei.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka tinakhota ndi kumayenda mokwera mtunda ndi njira yolowera ku Basani. Ndipo Ogi mfumu ya ku Basani ndi gulu lake lonse lankhondo anakumana nafe ndipo anamenyana nafe ku Ederi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo tinatembenuka, ndi kubwera kumka njira ya ku Basana; ndipo Ogi mfumu ya Basana anaturuka kukomana nafe, kugwirana nafe nkhondo, iye ndi anthu ace onse, ku Edrei.