Deuteronomy 3:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidalandanso mizinda yakumapiri, dziko lonse la Giliyadi ndi Basani, mpaka ku Saleka ndi Ederei, mizinda ya ufumu wa Ogi ku Basani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
midzi yonse ya kuchidikha, ndi Giliyadi lonse, ndi Basani lonse kufikira ku Saleka ndi Ederei, midzi ya dziko la Ogi m'Basani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tinalanda mizinda yonse ya ku mapiri, ku Giliyadi, Basani mpaka ku Saleka ndi Ederi, mizinda ya mu ufumu wa Ogi wa ku Basani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
midzi yonse ya kucidikha, ndi Gileadi lonse, ndi Basana lonse kufikira ku Saleka ndi Edrei, midzi ya dziko la Ogi m'Basana.