Deuteronomy 3:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Theka la fuko la Manase, ndidalipatsa dera lonse la Giliyadi limene lidatsalira, ndiponso Basani dziko la mfumu Ogi uja, ndiye kuti dera lonse la Arigobu. (Basani linkadziŵika ndi dzina loti dziko la Arefaimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi chotsalira cha Giliyadi, ndi Basani lonse, dziko la Ogi, ndinapatsa fuko la hafu la Manase; dziko lonse la Arigobu, pamodzi ndi Basani. (Ndilo lotchedwa dziko la Arefaimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Theka la fuko la Manase ndinalipatsa dziko lonse lotsala la Giliyadi ndi Basani yense yemwe ndi dera la ufumu wa Ogi. (Chigawo chonse cha Arigobu mu Basani chinkadziwika kuti ndi dziko la Arefai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi cotsalira ca Gileadi, ndi Basana lonse, dziko la Ogi, ndinapatsa pfuko la hafu la Manase; dziko lonse la Arigobi, pamodzi ndi Basana. (Ndilo lochedwa dziko la Arefai.