Deuteronomy 3:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akazi anu okha ndi ana anu adzakhalira m'mizinda imene ndidakupatsani, pamodzi ndi ng'ombe zanu zomwe. (Ndikudziŵa kuti muli ndi ng'ombe zambiri.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akazi anu, ndi ana anu, ndi zoweta zanu, (ndidziwa muli nazo zoweta zambiri), zikhale m'midzi yanu imene ndinakupatsani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma akazi anu, ana anu ndi ziweto zanu (ndikudziwa kuti muli ndi ziweto zambiri) zikhoza kumakhalabe mʼmizinda imene ndakupatsani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akazi anu, ndi ana anu, ndi zoweta zanu, (ndidziwa muli nazo zoweta zambiri), zikhale m'midzi yanu imene ndinakupatsani;