Deuteronomy 3:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, mundilole kuti ndingooloka mtsinje wa Yordani wokhawu, ndipo kuti ndiwone dziko labwinolo patsidyapo, dziko lokongola lamapiri, ndiponso mapiri a Lebanoni.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndioloketu, ndilione dziko lokomali lili tsidya la Yordani, mapiri okoma aja, ndi Lebanoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundilole ndipite ndi kukaona dziko labwinolo kutsidya kwa Yorodani dziko la mapiri abwinowo ndi Lebanoni.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndioloketu, ndilione dziko lokomali liri tsidya la Yordano, mapiri okoma aja, ndi Lebano.