Deuteronomy 3:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pa nthaŵi imeneyo mafumu aŵiri a Aamoriwo tidaŵalanda dziko patsidya pa Yordani, kuchokera ku chigwa cha mtsinje wa Arinoni mpaka ku phiri la Heremoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muja tinalanda dziko m'manja mwa mafumu awiri a Aamori okhala tsidya lija la Yordani, kuyambira mtsinje wa Arinoni kufikira phiri la Heremoni;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho pa nthawi imeneyi tinalanda kwa mafumu awiri Aamori, dera la kummawa kwa Yorodani, kuyambira ku khwawa la Arinoni mpaka ku Phiri la Herimoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muja tinalanda dziko m'manja mwa mafumu awiri a Aamori okhala tsidya lija la Yordano, kuyambira mtsinje wa Arinoni kufikira phiri la Herimoni;