Deuteronomy 3:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
(Asidoni potchula phiri la Heremoni ankati Sirioni, koma Aamori potchula phiri lomwelo ankati Seniri.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(Asidoni alitcha Heremoni Sirioni, koma Aamori alitcha Seniri);
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
(Asidoni amatcha Herimoni kuti Siriyoni, pamene Aamori amalitcha Seniri).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(Asidoni alicha Herimoni Sirioni, koma Aamori alicha Seniri);