Deuteronomy 30:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene adzakufikirani madalitso ndi matemberero amene ndatchula aja, mudzaŵakumbukira muli pakati pa mitundu ina kumaiko kumene Chauta, Mulungu wanu, adakumwazirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzakhala, zikakugwerani zonsezi, mdalitso ndi temberero, ndinaikazi pamaso panu, ndipo mukazikumbukira mumtima mwanu mwa amitundu onse, amene Yehova Mulungu wanu anakupirikitsiraniko;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madalitso ndi matemberero awa onse amene ndawayika pamaso panu akadzafika pa inu, inu nʼkukumbukira kulikonse kumene Yehova Mulungu wanu wakubalalitsirani pakati pa mitundu ya anthu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzakhala, zikakugwerani zonsezi, mdalitso ndi temberero, ndinaikazi pamaso panu, ndipo mukazikumbukila mumtima mwanu mwa amitundu onse, amene Yehova Mulungu wanu anakupitikitsiraniko;