Deuteronomy 30:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Silili kumwamba, kuti muzichita kudzifunsa kuti, “Kodi amene akwere kumwamba kukatitsitsira lamulo kuti tilimve, ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Silikhala m'mwamba, kuti mukati, Adzatikwerera m'mwamba ndani, ndi kubwera nalo kwa ife, ndi kutimvetsa ili, kuti tilichite?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sizili kumwamba, kuti muzichita kufunsa kuti, “Kodi ndani amene akwere kumwamba kuti akazitenge ndi kudzatilalikira kuti timvere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Silikhala m'mwamba, kuti mukati, Adzatikwerera m'mwamba ndani, ndi kubwera nalo kwa ife, ndi kutimvetsa ili, kuti tilicite?