Deuteronomy 30:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komanso silili pa tsidya la nyanja, kuti muthe kufunsa kuti, “Kodi amene aoloke nyanja kukatitengera lamulo kuti tilimve, ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo silikhala tsidya la nyanja, kuti mukati, Adzatiolokera ndani tsidya la nyanja, ndi kutitengera ili, ndi kutimvetsa ili, kuti tilichite?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso sizili pa tsidya la nyanja, kuti muzichita kufunsa kuti, “Kodi ndani amene adzawoloke nyanja kuti akatenge ndi kudzatilalikira kuti timvere?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo silikhala tsidya la nyanja, kuti mukati, Adzatiolokera ndani tsidya la nyanja, ndi kutitengera ili, ndi kutimvetsa ili, kuti tilicite?