Deuteronomy 30:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muli nalo pompano. Mukulidziŵa, mumalitchula ndipo mungathe kulitsata.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mauwa ali pafupifupi ndi inu, m'kamwa mwanu, ndi m'mtima mwanu, kuwachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ayi, mawu ali pafupi ndi inu; ali mʼkamwa mwanu ndi mu mtima mwanu kuti muwamvere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mauwa ali pafupifupi ndi inu, m'kamwa mwanu, ndi m'mtima mwanu, kuwacita.