Deuteronomy 30:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mukapanda kumvera, mukamakana kumva, m'malo mwake nkumatengeka kuti mupembedze milungu ina,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mukatembenukira mtima wanu, osamvera inu, nimukacheteka, ndi kugwadira milungu ina ndi kuitumikira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati mtima wanu udzatembenuka, inu nʼkukhala osandimvera, ndipo ngati mudzatengeka ndi kupita kukagwadira milungu ina ndi kuyipembedza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mukatembenukira mtima wanu, osamvera inu, nimukaceteka, ndi kugwadira milungu yina ndi kuitumikira;