Deuteronomy 30:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndikuchenjezeranitu tsopano kuti mudzaonongeka. Dziko ili la patsidya pa Yordani limene mukupita kukakhalamolo, simudzakhalitsamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndikulalikirani inu lero, kuti mudzatayika ndithu, masiku anu sadzachuluka m'dziko limene muolokera Yordani kulowamo kulilandira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
lero ndikulengeza kwa inu kuti mudzawonongeka ndithu. Simudzakhala nthawi yayitali mʼdziko limene mukulowamo pamene mukuwoloka Yorodani kuti mulitenge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndikulalikirani inu lero, kuti mudzatayika ndithu, masiku anu sadzacuruka m'dziko limene muolokera Yordano kulowamo kulilandira.