Deuteronomy 31:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi pa nthaŵi imeneyo ndidzaŵafulatira chifukwa cha machimo onse amene iwo adachita popembedza milungu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Ine ndidzabisatu nkhope yanga tsiku lija chifukwa cha zoipa zonse adazichita; popeza anadzitembenukira milungu ina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Ine ndidzabisa ndithu nkhope yanga pa tsiku limenelo chifukwa cha zoyipa zimene anachita potembenukira kwa milungu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Ine ndidzabisatu nkhope yanga tsiku lija cifukwa ca zoipa zonse adazicita; popeza anadzitembenukira milungu yina.