Deuteronomy 31:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsopano talemba nyimbo iyi. Uŵaphunzitse ndi kuŵalimbitsa Aisraele kuti idzakhale mboni yanga yoŵatsutsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano mudzilemberere nyimbo iyi, ndi kuphunzitsa ana a Israele iyi; muiike m'kamwa mwao, kuti nyimbo iyi indichitire mboni yotsutsa ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsopano ulembe mawu a nyimbo iyi ndipo uwaphunzitse Aisraeli, uwawuze kuti aziyimba, kuti ikhale mboni yanga yowatsutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano mudzilemberere nyimbo iyi, ndi kuphunzitsa ana a Israyeli iyi: mulike m'kamwa mwao, kuti nyimbo iyi indicitire mboni yotsutsa ana a Israyeli.