Deuteronomy 31:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tengani buku ili la malamulo a Mulungu, ndipo muliike pambali pa Bokosi lachipangano la Chauta, Mulungu wanu, kuti likhale kumeneko ngati mboni yokutsutsani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Landirani buku ili la chilamulo, nimuliike pambali pa likasa la chipangano la Yehova Mulungu wanu, likhale komweko mboni yakutsutsa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tengani Buku ili la Malamulo ndi kuliyika pambali pa Bokosi la Chipangano la Yehova Mulungu wanu. Likhale kumeneko ngati mboni yokutsutsani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Landirani buku ili la cilamulo, nimuliike pambali pa likasa la cipangano la Yehova Mulungu wanu, likhale komweko mboni yakutsutsa inu.