Deuteronomy 32:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lakumwamba, imva zimene ndikuti ndilankhule. Dziko lapansi imva mau a pakamwa panga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumwamba kutchere khutu, ndipo ndidzanena; ndi dziko lapansi limve mau a m'kamwa mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mverani, inu mayiko a mmwamba ndipo ine ndidzayankhula; imva, iwe dziko lapansi, mawu a pakamwa panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumwamba kuchere khutu, ndipo ndidzanena; Ndi dziko lapansi limve mau a m'kamwa mwanga;