Deuteronomy 32:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵapeza m'chipululu, kuthengo kwenikweni kopanda kanthu. Adaŵatchinjiriza, ndipo adaŵasamala, monga momwe akadasamalira diso lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anampeza m'dziko la mabwinja, m'chipululu cholira chopanda kanthu; anamzinga, anamlangiza, anamsunga ngati kamwana ka m'diso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamupeza mʼchipululu, ku malo owuma ndi kopanda kanthu. Anamuteteza ndi kumusamalira; anamutchinjiriza ngati mwanadiso wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anampeza m'dziko la mabwinja, ndi m'cipululu colira copanda kanthu; Anamzinga, anamlangiza, Anamsunga ngati kamwana lea m'diso;