Deuteronomy 32:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ataona zimenezi, adaŵakana anthuwo, chifukwa ana ao aamuna ndi aakazi adaautsa mkwiyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anachiona, nawanyoza, pakuipidwa nao ana ake amuna, ndi akazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anaona zimenezi ndipo anawakana chifukwa ana ake aamuna ndi aakazi anamukwiyitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anaciona, nawanyoza, Pakuipidwa nao ana ace amuna, ndi akazi.