Deuteronomy 32:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zophunzitsa zanga zigwe ngati mvula, mau anga atsike ngati mame, ngati mvula yowaza pa msipu wanthete, ngati mvula yamphamvu pa udzu watsopano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chiphunzitso changa chikhale ngati mvula; maneno anga agwe ngati mame; ngati mvula yowaza pamsipu, ndi monga madontho a mvula pazitsamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiphunzitso changa chigwe ngati mvula ndipo mawu anga atsike ngati mame, ngati mvumbi pa udzu watsopano, ngati mvula yochuluka pa zomera zanthete.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ciphunzitso canga cikhale ngati mvula; Maneno anga agwe ngati mame; Ngati mvula yowaza pamsipu, Ndi monga madontho a mvula pazitsamba.