Deuteronomy 32:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo wanga udzayaka ngati moto, udzafika mpaka ku dziko la anthu akufa. Udzatentha zonse pa dziko, udzapsereza ndi mapiri omwe mpaka m'tsinde mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti wayaka moto mu mkwiyo wanga, utentha kumanda kunsi ukutha dziko lapansi ndi zipatso zake, nuyatsa maziko a mapiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mkwiyo wanga wayaka ngati moto, umene umayaka mpaka ku dziko la anthu akufa. Motowo udzanyeketsa dziko lapansi ndi zokolola zake ndipo udzapsereza maziko a mapiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti wayaka moto mu mkwiyo wanga, Utentha kumanda kunsi Ukutha dziko lapansi ndi zipatso zace Nuyatsa maziko a mapiri,