Deuteronomy 32:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵaunjikira masoka osatha, mipaliro yanga yonse idzathera pa iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzawaunjikira zoipa; ndidzawathera mivi yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndidzawawunjikira masautso ndipo mivi yanga yonse idzathera pa iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzawaunjikira zoipa; Ndidzawathera nubvi yanga.