Deuteronomy 32:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achikhala ndidangoŵaononga kotheratu onsewo, kuti anthu pansi pano asaŵakumbukire ndi mmodzi yemwe!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinati, Ndikadawauzira ndithu, ndikadafafaniza chikumbukiro chao mwa anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinanena kuti ndidzawamwaza ndi kuwafafaniza kuti anthu asawakumbukirenso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinati, Ndikadawauzira ndithu, Ndikadafafaniza cikumbukiro cao mwa anthu;