Deuteronomy 32:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achikhala anzeru, akadamvetsa, ndipo akadazindikira zimene zitha kudzaŵagwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akadakhala nazo nzeru, akadazindikira ichi, akadasamalira chitsirizo chao!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati iwo akanakhala anzeru akanamvetsetsa izi ndi kuzindikira kuti mathero awo adzakhala otani!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akadakhala nazo nzeru, akadazindikira ici, Akadasamalira citsirizo cao!