Deuteronomy 32:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzatamanda dzina la Chauta. Tamandani ukulu wake wa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidzalalika dzina la Yehova. Nenani kuti Mulungu wathu ndi wamkulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzalalikira dzina la Yehova. Aa, tamandani ukulu wa Mulungu wathu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidzalalika dzina la Yehova; Nenani kuti Mulungu wathu ndi wamkulu.