Deuteronomy 32:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo Chauta adzafunsa anthu ake kuti, “Nanga milungu yamphamvu yomwe mumaikhulupirira ija ili kuti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo adzati, Ili kuti milungu yao, thanthwe limene anathawirako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzanena kuti, “Nanga ili kuti milungu yawo, thanthwe limene ankabisalamo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo adzati, Iri kuti milunguyao, Thanthwe limene anathawirako?