Deuteronomy 32:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukweza dzanja kumwamba, ndikulumbira pali Ine ndemwe wa moyo wosatha,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndikweza dzanja langa kuloza kumwamba, ndipo nditi, Pali moyo wanga kosatha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikweza dzanja langa kumwamba ndi kulumbira kuti, ‘Pali Ine wamoyo wamuyaya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndikweza dzanja langa kuloza kumwamba, Ndipo nditi, Pali moyo wanga kosatha,