Deuteronomy 32:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mivi yanga idzafiira ndi magazi ao ndipo lupanga langa lidzabayadi mnofu wao. Olasidwa ndi ogwidwa ukapolo magazi ao adzafalikadi, ndiponso mitu yao ya tsitsi litalilitali idzadulidwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mivi yanga ndiiledzeretsa nao mwazi, ndi lupanga langa lidzalusira nyama; ndi mwazi wa ophedwa ndi ogwidwa, ndi mutu wachitsitsi wa mdani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mivi yanga idzakhuta magazi awo pamene lupanga langa lidzawononga mnofu: magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa ukapolo, mitu ya atsogoleri a adani.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mibvi yanga ndiiledzeretsa nao mwazi, Ndi lupanga langa lidzalusira nyama; Ndi mwazi wa ophedwa ndi ogwidwa, Ndi mutu wacitsitsi wa mdani,