Deuteronomy 32:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose ndi Yoswa mwana wa Nuni adanena pamtima mau onse a nyimbo imeneyi, ndipo Aisraele ankamva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza Mose nanena mau onse a nyimbo iyi m'makutu mwa anthu, iye, ndi Yoswa mwana wa Nuni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anabwera ndi Yoswa mwana wa Nuni ndipo anayankhula mawu onsewa mʼnyimbo anthu akumva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza Mose nanena mau onse a nyimbo iyi m'makutu mwa anthu, iye, ndi Hoseya mwana wa Nuni.