Deuteronomy 32:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu ndinu osakhulupirika, osayenera kukhala anthu ake, ndinu mtundu wochimwa ndi wonyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamchitira zovunda si ndiwo ana ake, chilema nchao; iwo ndiwo mbadwo wopulukira ndi wokhotakhota.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iwo achita mosakhulupirika pamaso pake, iwo si ana akenso, koma iwo ndi mʼbado wachinyengo ndi wokhotakhota.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamcitira zobvunda si ndiwo ana ace, cirema ncao; Iwo ndiwo mbadwo wopulukira ndi wokhotakhota.