Deuteronomy 32:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake dziko limene ndikupatsa Aisraele uliwonere chapatali, koma kuloŵa kokha ndiye ai, suloŵamo”.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti udzapenya dzikoli pandunji pako; koma osalowako ku dziko limene ndipatsa ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho udzalionera kutali dziko limene ndikupereka kwa Aisraeli. Sudzalowa mʼdziko limene ndi kulipereka kwa Aisraeli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti udzapenya dzikoli pandunji pako; koma osalowako ku dziko limene ndipatsa ana a Israyeli.