Deuteronomy 32:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Wopambanazonse adapereka maiko kwa anthu a mitundu ina, pamene adalekanitsa anthu, adaŵaikira malire potsata kuchuluka kwa anthu a Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Wam'mwambamwamba anagawira amitundu cholowa chao, pamene anagawa ana a anthu, anaika malire a mitundu ya anthu, monga mwa kuwerenga kwao kwa ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Wammwambamwamba anapereka mayiko kwa anthu a mitundu ina kukhala cholowa chawo, pamene analekanitsa anthu onse, anayikira malire anthu onse molingana ndi chiwerengero cha ana a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Wam'mwambamwamba anagawira amitundu colowacao, Pamene anagawa ana a anthu, Anaika malire a mitundu ya anthu, Monga mwa kuwerenga kwao kwa ana a Israyeli,