Deuteronomy 33:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za fuko la Yosefe adati, “Chauta adalitse dziko lao, likhale la mvula yambiri, ndipo la zitsime zochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo za Yosefe anati, Yehova adalitse dziko lake; ndi zinthu zofunikatu za m'mwamba, ndi mame, ndi madzi okhala pansipo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za fuko la Yosefe anati: “Yehova adalitse dziko lake ndi mame ambiri ochokera kumwamba ndiponso madzi ambiri ochokera pansi pa nthaka;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo za Yosefe anati, Yehova adalitse dziko lace; Ndi zinthu zofunikatu za m'mwamba, ndi mame, Ndi madzi okhala pansipo;