Deuteronomy 33:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lao lidalitsidwe pokhala ndi zipatso zopsa ndi dzuŵa, likhalenso ndi zokolola zochuluka pa nyengo iliyonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zipatso zofunikatu za dzuwa, ndi zomera zofunikatu za mwezi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi zinthu zambiri zimene zimacha ndi dzuwa ndiponso ndi zokolola zabwino kwambiri zimene zimacha ndi mwezi uliwonse;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi zipatso zofunikatu za dzuwa, Ndi zomera zofunikatu za mwezi,