Deuteronomy 33:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapiri ao akalekaleŵa akutidwe ndi zipatso, ndipo adzazidwe ndi zokolola zochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zinthu zoposa za mapiri akale, ndi zinthu zofunikatu za zitunda zosatha,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi zipatso zabwino kwambiri zochokera mʼmapiri amakedzanawa ndiponso zokolola zochuluka zochokera ku zitunda zakalekale;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi zinthu zoposa za mapiri akale, Ndi zinthu zofunikatu za zitunda zosatha,