Deuteronomy 33:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku mapiri ao amaitanirako mitundu ya anthu, kumeneko amaperekako nsembe zoyenera, chifukwa choti amapeza chuma pochita malonda m'nyanja, kuchokera mu mchenga wa m'mbali mwa nyanja.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzaitana mitundu ya anthu afike kuphiri; apo adzaphera nsembe za chilungamo; popeza adzayamwa zochuluka za m'nyanja, ndi chuma chobisika mumchenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adzayitanira mitundu ya anthu kumapiri, kumeneko adzaperekako nsembe zachilungamo; kumeneko adzadyerera zinthu zochuluka zochokera ku nyanja, chuma chobisika mu mchenga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzaitana mitundu ya anthu afike kuphiri; Apo adzaphera nsembe za cilungamo; Popeza adzayamwa zocuruka za m'nyanja, Ndi cuma cobisika mumcenga.