Deuteronomy 33:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za fuko la Gadi, adati, “Alemekezeke Chauta amene adakulitsa dziko la Gadi. Gadi amalalira ngati mkango waukazi, amamwetula dzanja ndi bade la mutu lomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi za Gadi anati, Wodala iye amene akuza Gadi; akhala ngati mkango waukazi, namwetula dzanja, ndi pakati pa mutu pomwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za fuko la Gadi anati: “Wodala amene amakulitsa malire a Gadi! Gadi amakhala kumeneko ngati mkango, kukhadzula mkono kapena mutu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi za Gadi anati, Wodala iye amene akuza Gadi; Akhala ngati mkango waukazi, Namwetula dzanja, ndi pakati pa mutu pomwe.