Deuteronomy 33:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za fuko la Dani adati, “Dani ali ngati mwana wamkango, amene amalumpha kuchokera ku Basani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi za Dani anati, Dani ndiye mwana wa mkango, wakutumpha motuluka m'Basani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za fuko la Dani anati: “Dani ndi mwana wamkango, amene akutuluka ku Basani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi za Dani anati, Dani ndiye mwana wa mkango, Wakutumpha moturuka m'Basana.