Deuteronomy 33:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za fuko la Asere, adati, “Asere ndi wodalitsidwa kupambana mafuko ena. Abale ake amkonde, dziko lake likhale lachuma, la mitengo ya olivi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi za Asere anati, Asere adalitsidwe mwa anawo; akhale wovomerezeka mwa abale ake, aviike phazi lake m'mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za fuko la Aseri anati: “Mwana wodalitsika kwambiri ndi Aseri; abale ake amukomere mtima, ndipo asambe mapazi ake mʼmafuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi za Aseri anati, Aseri adalitsidwe mwa anawo; Akhale wobvomerezeka mwa abale ace, Abviike phazi lace m'mafuta.