Deuteronomy 33:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Midzi yake itchinjirizidwe ndi zitseko zachitsulo m'malinga, mphamvu zake zikhalitse monga masiku a moyo wake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsapato zako zikhale za chitsulo ndi mkuwa; ndipo monga masiku ako momwemo mphamvu yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zotsekera za zipata zako zidzakhala za chitsulo ndi za mkuwa, ndi mphamvu zako zidzakhala ngati masiku a moyo wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsapato zako zikhale za citsulo ndi mkuwa; Ndipo monga masiku ako momwemo mphamvu yako.