Deuteronomy 33:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adakhala mfumu ya anthu ake Aisraele, pamene mafuko ao ndi atsogoleri ao adasonkhanitsidwa pamodzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anali mfumu m'Yesuruni, pakusonkhana mafumu a anthu, pamodzi ndi mafuko a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anali mfumu ya Yesuruni pamene atsogoleri a anthu anasonkhana, pamodzi ndi mafuko a Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anali mfumu m'Yesuruni, Pakusonkhana mafumu a anthu, Pamodzi ndi mapfuko a Israyeli.