Deuteronomy 33:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ponena za fuko la Rubeni, Mose adati, “Rubeni asafafanizike, akhalitse ndithu, ngakhale anthu ake ali pang'ono.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Rubeni akhale ndi moyo, asafe, koma amuna ake akhale owerengeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Lolani Rubeni akhale ndi moyo ndipo asafe, anthu ake asachepe pa chiwerengero.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Rubeni akhale ndi moyo, asafe, Koma amuna ace akhale owerengeka.