Deuteronomy 33:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za fuko la Levi adati, “Inu Chauta, Tumimu ndi Urimu adziŵitse kufuna kwanu kudzera mwa Alevi, atumiki anu okhulupirika. Mudaŵayesa ku Masa kuja, ndipo mudalimbana nawo ku madzi a Meriba kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo za Levi anati, Tumimu ndi Urimu wanu zikhala ndi wokondedwa wanu, amene mudamuyesa m'Masa, amene mudalimbana naye ku madzi a Meriba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za fuko la Alevi anati: “Tumimu wanu ndi Urimu ndi za mtumiki wanu wokhulupirika. Munamuyesa ku Masa; munalimbana naye ku madzi a ku Meriba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo za Levi anati, Tumimu ndi Urimu wanu zikhala ndi wokondedwa wanu, Amene mudamuyesa m'Masa, Amene mudalimbana naye ku madzi a Meriba;