Deuteronomy 34:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamuwonetsanso chigawo chakumwera cha Negebu, ndi chigwa chimene chimafika mpaka ku Yeriko, mzinda wa mitengo ya migwalangwa, mpaka ku Zowari.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kumwera, ndi chidikha cha chigwa cha Yeriko, mudzi wa migwalangwa, kufikira ku Zowari.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Negevi ndi chigawo chonse kuchokera ku Chigwa cha Yeriko, Mzinda wa mitengo ya migwalangwa, mpaka ku Zowari.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kumwela, ndi cidikha eli cigwa ca Yeriko, mudzi wa migwalangwa, kufikira ku Zoari.