Deuteronomy 34:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele adalira maliro ake masiku makumi atatu m'chigwa cha Mowabu. Ndipo nthaŵi yolira maliro idatha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele analira Mose m'zidikha za Mowabu masiku makumi atatu; potero anatha masiku akulira maliro a Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli analira maliro a Mose mʼchikhwawa cha Mowabu kwa masiku makumi atatu mpaka nthawi ya kulira maliro ndi kukhuza inatha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli analira Mose m'zidikha za Moabu masiku makumi atatu; potero anatha masiku akulira maliro a Mose.