Deuteronomy 4:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandilamula nthaŵi imeneyo kuti ndikuphunzitseni malamulo amene muyenera kumaŵasunga m'dziko limene mukaloŵe ndi kukakhalamolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anandilamulira muja ndikuphunzitseni malemba ndi maweruzo, kuti mukawachite m'dziko limene muolokerako kulilandira likhale lanulanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anandilamula nthawi imene ija kuti ndikuphunzitseni malangizo ndi malamulo amene muyenera kutsata mʼdziko limene mutenge mukawoloka Yorodani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anandilamulira muja ndikuphunzitseni malemba ndi maweruzo, kuti mukawacite m'dziko limene muolokerako kulilandira likhale lanu lanu.