Deuteronomy 4:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Samalani kuti musachimwe pakudzipangira fano la mtundu uliwonse, kaya fanolo likhale longa mwamuna kaya mkazi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mungadziipse, ndi kudzipangira fano losema, lakunga chifaniziro chilichonse, mafanidwe a mwamuna kapena mkazi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti musasokonezeke ndi kudzipangira nokha fano kapena chifanizo cha mtundu uliwonse, kaya chokhala ngati mwamuna kapena ngati mkazi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mungadziipse, ndi kudzipangira fano losema, lakunga cifaniziro ciri conse, mafanidwe a mwamuna kapena mkazi;