Deuteronomy 4:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
fano la nyama iliyonse ya pa dziko lapansi, fano la mbalame iliyonse yamumlengalenga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mafanidwe a nyama iliyonse ili pa dziko lapansi, mafanidwe a mbalame iliyonse yamapiko yakuuluka m'mlengalenga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kaya chokhala ngati nyama iliyonse ya pa dziko lapansi kapena mbalame iliyonse yowuluka mlengalenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mafanidwe a nyama iri yonse iri pa dziko lapansi, mafanidwe a mbalame iri yonse yamapiko yakuuluka m'mlengalenga,