Deuteronomy 4:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzafera m'dziko lomwe lino osaoloka mtsinjewo. Koma inu, muli pafupifupi kuwoloka ndi kukhala m'dziko lokomalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti ndidzafa m'dziko muno, osaoloka Yordani; koma inu mudzaoloka, ndi kulandira dziko ili lokoma likhale lanulanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndifera mʼdziko lino, sindiwoloka Yorodani. Koma inu mwatsala pangʼono kuwoloka ndi kukatenga dziko labwinolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti ndidzafa m'dziko muno, osaoloka Yordano; koma inu mudzaoloka, ndi kulandira dziko ili lokoma likhale lanu lanu.