Deuteronomy 4:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukadzakhala pa mavuto, ndipo zinthu zonsezi nkukuchitikirani, pamenepo mudzabwerera kwa Chauta, Mulungu wanu, ndipo mudzamvera mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukakhala nao msauko, zikakugwerani zonsezi, masiku otsiriza mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndi kumvera mau ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukadzakhala pa chipsinjo ndipo zonsezi zikadzakuchitikirani, ndi pamene pambuyo pake mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndi kumumvera Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukakhala nao msauko, zikakugwerani zonsezi, masiku otsiriza mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndi kumvera mau ace;